27 Ndipo unamtsata unyinji waukuru wa anthu, ndi wa akazi amene anadziguguda pacifuwa, namlirira iye.
Werengani mutu wathunthu Luka 23
Onani Luka 23:27 nkhani