Luka 23:34 BL92

34 Ndipo Yesu ananena, Atate, muwakhululukire iwo, pakuti sadziwa cimene acita. Ndipo anagawana zobvala zace, poyesa maere.

Werengani mutu wathunthu Luka 23

Onani Luka 23:34 nkhani