Luka 23:47 BL92

47 Ndipo 2 pamene kenturiyo anaona cinacitikaco, analemekeza Mulungu, nanena, Zoonadi munthu uyu anali wolungama.

Werengani mutu wathunthu Luka 23

Onani Luka 23:47 nkhani