Luka 24:17 BL92

17 Ndipo anati kwa iwo, Mau awa ndi otani mulandizanawo poyendayenda? Ndipo anaima ndi nkhope zao zacisoni.

Werengani mutu wathunthu Luka 24

Onani Luka 24:17 nkhani