Luka 24:49 BL92

49 Ndipo onani, 12 Ine nditumiza pa inu lonjezano la Atate wanga; koma khalani inu m'mudzi muno, kufikira mwabvekedwa ndi mphamvu yocokera Kumwamba.

Werengani mutu wathunthu Luka 24

Onani Luka 24:49 nkhani