Luka 4:13 BL92

13 Ndipo mdierekezi, m'mene adamariza mayesero onse, analekana naye kufikira nthawi yina.

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:13 nkhani