Luka 4:14 BL92

14 Ndipo Yesu anabwera ndi mphamvu ya Mzimu ku Galileya; ndipo mbiri yace ya iye inabuka ku dziko lonse loyandikira.

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:14 nkhani