Luka 5:15 BL92

15 Koma makamaka mbiri yace ya iye inabuka: ndipo mipingo yambiri ya anthu inasonkhanakudzamvera, ndi kudzaciritsidwa nthenda zao.

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:15 nkhani