Luka 6:8 BL92

8 Koma iye anadziwa maganizo ao; nati kwa munthuyo wa dzanja lace lopuwala, Nyamuka, nuimirire pakatipo.

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:8 nkhani