Luka 9:1 BL92

1 Ndipo iye anaitana pamodzi khumi ndi awiriwo nawapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse, ndi zakuciritsa nthenda.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:1 nkhani