1 Mbiri 1:32 BL92

32 Ndi ana a Ketura mkazi wamng'ono wa Abrahamu anabala Zimiramu, ndi Yokisani, ndi Medani, ndi Midyani, ndi Isibaki, ndi Sua. Ndi ana a Yokisani: Seba, ndi Dedani.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 1

Onani 1 Mbiri 1:32 nkhani