43 Mafumu tsono akucita ufumu m'dziko la Edomu, pakalibe mfumu wakucita ufumu pa ana a Israyeli, ndiwo Bela mwana wa Beori; ndi dzina la mudzi wace ndilo Dinaba.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 1
Onani 1 Mbiri 1:43 nkhani