1 Mbiri 10:4 BL92

4 Pamenepo Sauli anati kwa wonyamula zida zace, Solola lupanga lako, nundipyoze nalo, angafike osadulidwa awa ndi kundiseka, Koma wonyamula zida zace anakana, popeza anaopa kwambiri. Pomwepo Sauli anatenga lupanga lace, naligwera.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 10

Onani 1 Mbiri 10:4 nkhani