1 Mbiri 10:8 BL92

8 Ndipo m'mawa mwace anafika Afilisti kubvula za ophedwa, napeza Sauli ndi ana ace adagwa pa phiri la Giliboa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 10

Onani 1 Mbiri 10:8 nkhani