1 Mbiri 11:1 BL92

1 Pamenepo Aisrayeli onse anasonkhana kwa Davide ku Hebroni, ndi kuti, Taonani, ife ndife pfupa lanu, ndi mnofu wanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:1 nkhani