1 Mbiri 11:23 BL92

23 Anaphanso M-aigupto munthu wamkuru, msinkhu wace mikono isanu, ndi m'dzanja la M-aigupto munali mkondo ngati mtanda woombera nsaru; ndipo anamtsikira ndi ndodo, nakwatula mkondo m'dzanja la M-aigupto, namupha ndi mkondo wace womwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11

Onani 1 Mbiri 11:23 nkhani