8 Ndipo anamanga mudzi pozungulira pace, kuyambira ku Milo ndi pozungulira pace; ndi Yoabu anakonzanso potsala pa mudzi.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 11
Onani 1 Mbiri 11:8 nkhani