1 Mbiri 12:1 BL92

1 Anadzawo kwa Davide ku Zikilaga, akali citsekedwere cifukwa ca Sauli mwana wa Kisi, ndi awa; ndiwo mwa amphamvuwo omthandiza kunkhondo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:1 nkhani