11 Ndipo kudaipira Davide kuti Yehova adacita cipasulo ndi Uza; motero anacha malowo Perezi Uza, mpaka lero lino.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 13
Onani 1 Mbiri 13:11 nkhani