1 Mbiri 13:2 BL92

2 Ndipo Davide anati kwa msonkhano wonse wa Israyeli, Cikakomera inu, ndipo cikacokera kwa Yehova Mulungu wathu, titumize konse kuti abale athu otsala m'dziko lonse la Israyeli, ndi ansembe ndi Alevi okhala nao m'midzi yao yokhala napa podyetsa, kuti asonkhane kwa ife;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 13

Onani 1 Mbiri 13:2 nkhani