1 Mbiri 15:26 BL92

26 Ndipo popeza Mulungu anathandiza Alevi akusenza likasa la cipangano la Yehova, iwo anapha nsembe ng'ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 15

Onani 1 Mbiri 15:26 nkhani