1 Mbiri 16:10 BL92

10 Mudzitamandire ndi dzina lace lopatulika;Mitima yao ya iwo ofuna Yehova ikondwere.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 16

Onani 1 Mbiri 16:10 nkhani