1 Mbiri 16:30 BL92

30 Njenjemerani pamaso pace, inu dziko lonse lapansi,Dziko lokhalamo anthu lomwe lakhazikika, kuti silingagwedezeke.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 16

Onani 1 Mbiri 16:30 nkhani