1 Mbiri 16:4 BL92

4 Ndipo anaika Alevi ena atumikire ku likasa la Yehova, nalalikire, nayamike, nalemekeze Yehova Mulungu wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 16

Onani 1 Mbiri 16:4 nkhani