1 Mbiri 16:41 BL92

41 ndi pamodzi nao Hemani, ndi Yedutuni, ndi osankhika otsalawo, ochulidwa maina, kuyamika Yehova; pakuti cifundo cace ncosatha;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 16

Onani 1 Mbiri 16:41 nkhani