1 Mbiri 18:5 BL92

5 Ndipo Aaramu a ku Damasiko anadza kudzathandiza Hadarezeri mfumu ya Zoba; koma Davide anakantha Aaramu amuna zikwi makumi awiri mphambu ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 18

Onani 1 Mbiri 18:5 nkhani