1 Mbiri 18:8 BL92

8 Ndi ku Tibati, ndi ku Kuni, midzi ya Hadarezeri, Davide anatenga mkuwa wambiri, ndiwo umene Solomo anayenga nao thawale lamkuwa, ndi nsanamira, ndi zipangizo zamkuwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 18

Onani 1 Mbiri 18:8 nkhani