12 Ndipo anati, Akandilaka Aaramu, udzandilanditsa ndiwe; koma akakulaka ana a Amoni, ndidzakulanditsa ndine.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19
Onani 1 Mbiri 19:12 nkhani