1 Mbiri 19:7 BL92

7 Momwemo anadzilembera magareta zikwi makumi atatu mphambu ziwiri, ndi mfumu ya Maaka ndi anthu ace; nadza iwo, namanga misasa cakuno ca Medeba. Ana a Amoni omwe anasonkhana m'midzi mwao, nadza kunkhondo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19

Onani 1 Mbiri 19:7 nkhani