1 Mbiri 2:16 BL92

16 ndi alongo ao ndiwo Zeruya ndi Abigaili. Ndi ana a Zeruya: Abisai ndi Yoabu, ndi Asaheli; atatu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2

Onani 1 Mbiri 2:16 nkhani