23 Ndi Gesuri ndi Aramu analanda midzi ya Yairi, pamodzi ndi Kenati ndi miraga yace; ndiyo midzi makumi asanu ndi limodzi. Iwo onse ndiwo ana a Makiri atate wa Gileadi.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2
Onani 1 Mbiri 2:23 nkhani