1 Mbiri 2:3 BL92

3 Ana a Yuda ndiwo Eri, ndi Onani, ndi Sela; Batisua Mkanani anambalira atatu amenewa. Koma Eri mwana woyamba wa Yuda anali woipa pamaso pa Yehova, ndi iye anamupha.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2

Onani 1 Mbiri 2:3 nkhani