42 Ndi ana a Kalebi mbale wa Yerameli ndiwo Mesa mwana wace woyamba, ndiye atate wa Zifi; ndi ana a Maresa atate wa Hebroni.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2
Onani 1 Mbiri 2:42 nkhani