49 Iyeyu anabalanso Safa atate wa Madimana, Seva atate wa Makibena, ndi atate wa Gibeya; ndi mwana wamkazi wa Kalebi ndiye Akisa.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2
Onani 1 Mbiri 2:49 nkhani