1 Mbiri 20:4 BL92

4 Ndipo zitatha izi, inauka nkhondo ku Gezeri ndi Afilisti; pamenepo Sibekai Mhusati anapha Sipai wa ana a cimphona; ndipo anawagonjetsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 20

Onani 1 Mbiri 20:4 nkhani