1 Mbiri 20:7 BL92

7 Ndipo potonza Israyeli iyeyu Yonatani mwana wa Simeya mbale wace wa Davide anamkantha.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 20

Onani 1 Mbiri 20:7 nkhani