29 Pakuti kacisi wa Yehova amene Mose anapanga m'cipululu, ndi guwa la nsembe yopsereza, zinali pa msanje wa ku Gibeoni nthawi yomweyi.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21
Onani 1 Mbiri 21:29 nkhani