1 Mbiri 21:5 BL92

5 Ndipo Yoabu anapereka kwa Davide ciwerengo ca anthu owerengedwa. Ndipo Aisrayeli onse anali zikwi mazana khumi ndi limodzi osolola lupanga, ndi Yuda anali zikwi mazana anai mphambu makumi asanu ndi awiri akusolola lupanga,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21

Onani 1 Mbiri 21:5 nkhani