1 Mbiri 21:8 BL92

8 Pamenepo Davide anati kwa Mulungu, Ndacimwa kwakukuru ndi kucita cinthu ici; koma tsopano, mucotse mphulupulu ya kapolo wanu, pakuti ndacita kopusa ndithu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21

Onani 1 Mbiri 21:8 nkhani