13 Momwemo udzalemerera, ukasamalira kucita malemba ndi maweruzo amene Yehova analangiza Mose za Israyeli; limbikatu, nulimbike mtima, usaope, usade mtima.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 22
Onani 1 Mbiri 22:13 nkhani