1 Mbiri 22:3 BL92

3 Nakonzeratu Davide citsulo cocuruka ca misomali ya ku zitseko za zipata, ndi ya kuphatikizitsa; ndi mkuwa wocuruka wosauyesa kulemera kwace;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 22

Onani 1 Mbiri 22:3 nkhani