1 Mbiri 22:5 BL92

5 Ndipo Davide anati, Solomo mwana wanga ndiye mnyamata ndi wosakwima, ndi nyumba imene adzaimangira Yehova ikhale yaikuru yopambana, yomveka ndi ya ulemerero mwa maiko onse; ndiikonzeretu mirimo. Momwemo Davide anakonzeratu mocuruka asanamwalire.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 22

Onani 1 Mbiri 22:5 nkhani