1 Mbiri 22:7 BL92

7 Ndipo Davide anati kwa Solomo mwana wace, Kunena za ine, kumtima kwanga kudati, ndilimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 22

Onani 1 Mbiri 22:7 nkhani