1 Mbiri 23:11 BL92

11 Wamkuru wa iwo ndi Yahati, mnzace ndi Ziza; koma Yeusi ndi Beriya analibe ana ambiri, potero anakhala nyumba ya kholo yowerengedwa pamodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 23

Onani 1 Mbiri 23:11 nkhani