1 Mbiri 23:29 BL92

29 ya mkate woonekera womwe, ndi ya ufa wosalala wa nsembe yaufa, ndi ya timitanda taphanthiphanthi topanda cotupitsa, ndi ya ciwaya, ndi yakukazinga, ndi ya miyeso iri yonse;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 23

Onani 1 Mbiri 23:29 nkhani