1 Mbiri 23:4 BL92

4 A iwowa zikwi makumi awiri mphambu zinai anayang'anira nchito ya nyumba ya Yehova, ndi zikwi zisanu ndi cimodzi ndiwo akapitao ndi oweruza,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 23

Onani 1 Mbiri 23:4 nkhani