1 Mbiri 23:9 BL92

9 Ana a Simeyi: Selomoti, ndi Hazieli, ndi Hanani; atatu. Ndiwo akuru a nyumba za makolo a Ladani.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 23

Onani 1 Mbiri 23:9 nkhani