1 Mbiri 24:1 BL92

1 Ndipo magawidwe a ana a Aroni ndi awa. Ana a Aroni: Nadabu, ndi Abihu, Eleazara, ndi Itamara.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 24

Onani 1 Mbiri 24:1 nkhani