1 Mbiri 24:19 BL92

19 Awa ndi malongosoledwe ao m'utumiki wao kulowa m'nyumba ya Yehova, monga mwa ciweruzo adawapatsa Aroni atate wao, monga Yehova Mulungu wa Israyeli anamlamulira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 24

Onani 1 Mbiri 24:19 nkhani