1 Mbiri 26:10 BL92

10 Hosa yemwe wa ana a Merari anali ndi ana, wamkuru ndi Simri; pakuti ngakhale sanali wobadwa woyamba, atate wace anamuyesa wamkuru;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:10 nkhani